Ndili ndi tecno spark 5 for sale! Koma ali ndi mavuto ochepa chabe.
1. Battery limangokhala 3 minutes
2. Charging system inafoila, ndimagwiritsa ntchito multicharger
3. Earpiece imamveka mazenene
4. Mouthpiece imafunika kuimenya pang'ono usanaimbe or kuyankha foni
5. Button la 2, and 7 silimagwira
6. Camera yasiya kugwira dzulodzuloli
7. Lcd imaonetsa timizere
8. Network imathawathawa
9. Internet inasiya
10. Face ndiyofunika kusintha
11. Imathimathima I think ili ndi ka virus kofunika kungochotsetsa
12. Vibration inasiya kugwira.
Are you interested? Hit my inbox, serious buyers only.🤣