Ndili ndi tecno spark 5 for sale! Koma ali ndi mavuto ochepa chabe.
1. Battery limangokhala 3 minutes
2. Charging system inafoila, ndimagwiritsa ntchito multicharger
3. Earpiece imamveka mazenene
4. Mouthpiece imafunika kuimenya pang'ono usanaimbe or kuyankha foni
5. Button la 2, and 7 silimagwira
6. Camera yasiya kugwira dzulodzuloli
7. Lcd imaonetsa timizere
8. Network imathawathawa
9. Internet inasiya
10. Face ndiyofunika kusintha
11. Imathimathima I think ili ndi ka virus kofunika kungochotsetsa
12. Vibration inasiya kugwira.
Are you interested? Hit my inbox, serious buyers only.🤣
Ndili ndi tecno spark 5 for sale! Koma ali ndi mavuto ochepa chabe. 1. Battery limangokhala 3 minutes 2. Charging system inafoila, ndimagwiritsa ntchito multicharger 3. Earpiece imamveka mazenene 4. Mouthpiece imafunika kuimenya pang'ono usanaimbe or kuyankha foni 5. Button la 2, and 7 silimagwira 6. Camera yasiya kugwira dzulodzuloli 7. Lcd imaonetsa timizere 8. Network imathawathawa 9. Internet inasiya 10. Face ndiyofunika kusintha 11. Imathimathima I think ili ndi ka virus kofunika kungochotsetsa 12. Vibration inasiya kugwira. Are you interested? Hit my inbox, serious buyers only.🤣
Like
Haha
4
0 Comments 0 Shares 187 Views 0 Reviews