ZILU
Mises à jour récentes
  • Nkhani pano ndyakutu kwavuta uku .samalani Amene akudutsa nseu wa Machinjiri Area 1 ayitchole. Sitima yafa ndipo yatseka nseu.

    Pakadali pano amene amayenda akumakwawa kudutsa pansi pa sitima po, amene adali pa njinga yamoto akumalipila aganyu pompo kuti awanyamulile njinga ayike mbali inayo, ndipo amagalimoto akuyitchola
    #ZILU
    Nkhani pano ndyakutu kwavuta uku .samalani Amene akudutsa nseu wa Machinjiri Area 1 ayitchole. Sitima yafa ndipo yatseka nseu. Pakadali pano amene amayenda akumakwawa kudutsa pansi pa sitima po, amene adali pa njinga yamoto akumalipila aganyu pompo kuti awanyamulile njinga ayike mbali inayo, ndipo amagalimoto akuyitchola #ZILU
    Like
    1
    0 Commentaires 0 Parts 457 Vue 0 Aperçu
  • BREAKING

    Chimwemwe Idana wathawa ku Silver Strikers pomwe tsopano wamvana zonse zobwereranso ku FCB Nyasa Big Bullets.

    Akuluakulu a ku Maule ati osewerayu amawapwetekabe kutengera ntchito yomwe amagwira ndipo anakambirana naye mseli pomwe matimuwa anakumana mu Charity Shield.

    Padakali pano, Idana waonedwa akuzungulira ku Blantyre ndipo ayamba nawo zokonzekera ndi timu ya Bullets chifukwa analibe mgwirizano ku Silver.

    #ZILU
    BREAKING Chimwemwe Idana wathawa ku Silver Strikers pomwe tsopano wamvana zonse zobwereranso ku FCB Nyasa Big Bullets. Akuluakulu a ku Maule ati osewerayu amawapwetekabe kutengera ntchito yomwe amagwira ndipo anakambirana naye mseli pomwe matimuwa anakumana mu Charity Shield. Padakali pano, Idana waonedwa akuzungulira ku Blantyre ndipo ayamba nawo zokonzekera ndi timu ya Bullets chifukwa analibe mgwirizano ku Silver. #ZILU
    Like
    1
    0 Commentaires 0 Parts 459 Vue 0 Aperçu
  • GABA NETS A WINNER FOR SWALLOWS

    Gabadinho Mhango scored a vital goal for Swallows on 90th minute as they beat Cape Town Spurs 1-0 in the DSTV Premiership on Sunday in South Africa.

    Mhango was trusted to start after returning from national team and caused some havoc for the home side before shown a yellow card on 88th minute and had to respond with a goal just seconds later.

    The win has taken Swallows up to 13th with 23 points in the league and Mhango has now three goals for the season.

    Reported by Hastings Wadza Kasonga Jr
    GABA NETS A WINNER FOR SWALLOWS Gabadinho Mhango scored a vital goal for Swallows on 90th minute as they beat Cape Town Spurs 1-0 in the DSTV Premiership on Sunday in South Africa. Mhango was trusted to start after returning from national team and caused some havoc for the home side before shown a yellow card on 88th minute and had to respond with a goal just seconds later. The win has taken Swallows up to 13th with 23 points in the league and Mhango has now three goals for the season. Reported by Hastings Wadza Kasonga Jr
    Like
    1
    1 Commentaires 0 Parts 276 Vue 0 Aperçu
  • If you want someone for decorations on your
    Birthdays
    Weddings
    Bridal shower
    And other events

    Here come Moshu Chipwere
    Takambilana nayeni ngati mukufuna zinthu zapamwamba🙂
    If you want someone for decorations on your Birthdays Weddings Bridal shower And other events Here come [MoshuMafiaChipwere] Takambilana nayeni ngati mukufuna zinthu zapamwamba🙂
    Love
    1
    1 Commentaires 0 Parts 622 Vue 0 Aperçu
  • Kd mwakolola kale Kwanuko??
    Kd mwakolola kale Kwanuko??
    Like
    1
    1 Commentaires 0 Parts 268 Vue 0 Aperçu
  • Mwafika paja pomati ipatse moto ntchalitchi🙏?
    Mwafika paja pomati ipatse moto ntchalitchi🙏?
    Love
    1
    0 Commentaires 0 Parts 290 Vue 0 Aperçu
Plus de lecture