BREAKING

Chimwemwe Idana wathawa ku Silver Strikers pomwe tsopano wamvana zonse zobwereranso ku FCB Nyasa Big Bullets.

Akuluakulu a ku Maule ati osewerayu amawapwetekabe kutengera ntchito yomwe amagwira ndipo anakambirana naye mseli pomwe matimuwa anakumana mu Charity Shield.

Padakali pano, Idana waonedwa akuzungulira ku Blantyre ndipo ayamba nawo zokonzekera ndi timu ya Bullets chifukwa analibe mgwirizano ku Silver.

#ZILU
BREAKING Chimwemwe Idana wathawa ku Silver Strikers pomwe tsopano wamvana zonse zobwereranso ku FCB Nyasa Big Bullets. Akuluakulu a ku Maule ati osewerayu amawapwetekabe kutengera ntchito yomwe amagwira ndipo anakambirana naye mseli pomwe matimuwa anakumana mu Charity Shield. Padakali pano, Idana waonedwa akuzungulira ku Blantyre ndipo ayamba nawo zokonzekera ndi timu ya Bullets chifukwa analibe mgwirizano ku Silver. #ZILU
Like
1
0 Reacties 0 aandelen 469 Views 0 voorbeeld