Nkhani pano ndyakutu kwavuta uku .samalani Amene akudutsa nseu wa Machinjiri Area 1 ayitchole. Sitima yafa ndipo yatseka nseu.

Pakadali pano amene amayenda akumakwawa kudutsa pansi pa sitima po, amene adali pa njinga yamoto akumalipila aganyu pompo kuti awanyamulile njinga ayike mbali inayo, ndipo amagalimoto akuyitchola
#ZILU
Nkhani pano ndyakutu kwavuta uku .samalani Amene akudutsa nseu wa Machinjiri Area 1 ayitchole. Sitima yafa ndipo yatseka nseu. Pakadali pano amene amayenda akumakwawa kudutsa pansi pa sitima po, amene adali pa njinga yamoto akumalipila aganyu pompo kuti awanyamulile njinga ayike mbali inayo, ndipo amagalimoto akuyitchola #ZILU
Like
1
0 Kommentare 0 Anteile 471 Ansichten 0 Vorschau