KODI MUKUDZIWA??

```Phosomthumba``` ✍️

1. Pali kampani ina ku USA imene ikuti ipeleka $10, 000 (16,825,598.91 MWK) kwa munthu amene atakhale mwezi osasewelesa foni yake.

2. Ubongo wathu umayamba kukhwinyika (shrink) tikamafika zaka za m'mma 30s/40s.

3. Anonychia ndi medical condition imene munthu amabadwa, kukula opanda zikhadabo.

4. Chocolate, cheese komanso red wine ati zimathandiza kuti munthu akhale ndi moyo wautali. A science amatelo.

5. Ku India kuli temple inayake imene galu amapeleka madalitso anthu akamutuluka mu temple'mu.

6. Munthu olemera kwambiri padziko lonse lapansi anali Mansa Musa ndipo chuma chake kufikila lero palibe amayandikilako $400, 000, 000, 000.

7. Acid amene amapezeka m'mimba mwathu ali ndi kuthekela kosungunla lezala.

8. Mtengo wa machineel ndi mtengo oopsa kwambiri dontho (khambi) lake likhoza kubwelesa zilonda zopweteka kwambiri, kudya chipaso chamuntengowu umafelatu. Utati uyesele kuotcha mtengowu utsi okhawo wa mtengowo umapangisa munthu kusiya kuona.

9. Dziko ndi planet yokhayo imene moto umatha kuyaka. Ma planet enawo nzosatheka chifukwa kulibe oxygen okwanila.

10. Mudzi wina ku Germany, Fuggerei rent sinakwelebe kuchokela 1520. Ndi $1 pachaka (pafupifupi 1800MWK).

11. Mukasecha pa Google kuti "DO A BARELL ROLL" page yonse imazungulira (spinning).

12. China yatulutsa battery ya nuclear imene ukaika mu phone mwanumo, ndiye kuti patha zaka 50 musanatchaje🥱.

13. Nyerere zimagona pafupifupi 9hours patsiku,kuonjezela apo izozi zili ndi mimba ziwiri ina yosungila zakudya zake ina zokudya za amzake.

14. Njoka zazikazi zimatha kusunga ma sperm a amuna kwa zaka 5, amuna ambiri akhoza kugonana ndi njoka zazikazi koma izo zimangolandila ma sperm'wo kumasunga then zimapanga decide kuti nah masperm awa okha agwire ntchito.

15. Malovu athu amakhala ndi ma pathogens amene akhoza kupha mbalame, eya mbalame. Malovu athuwa ndi a toxic kwa zinyama zina monga mbalame. Mbalame itati yachita soka kutela pamlomo kugundana ndi malovu athu, eh! Pamakhala chiopsezo chachikulu kuti ifa chifukwa malovu athu amakhala ndi ma bacteria omwe amapangisa mbalame kumangoyasamula, kukhosomola kwambiri then imafa...



Copied from star warelo ```Phosomthumba``` ✍️
KODI MUKUDZIWA?? ```Phosomthumba``` ✍️ 1. Pali kampani ina ku USA imene ikuti ipeleka $10, 000 (16,825,598.91 MWK) kwa munthu amene atakhale mwezi osasewelesa foni yake. 2. Ubongo wathu umayamba kukhwinyika (shrink) tikamafika zaka za m'mma 30s/40s. 3. Anonychia ndi medical condition imene munthu amabadwa, kukula opanda zikhadabo. 4. Chocolate, cheese komanso red wine ati zimathandiza kuti munthu akhale ndi moyo wautali. A science amatelo. 5. Ku India kuli temple inayake imene galu amapeleka madalitso anthu akamutuluka mu temple'mu. 6. Munthu olemera kwambiri padziko lonse lapansi anali Mansa Musa ndipo chuma chake kufikila lero palibe amayandikilako $400, 000, 000, 000. 7. Acid amene amapezeka m'mimba mwathu ali ndi kuthekela kosungunla lezala. 8. Mtengo wa machineel ndi mtengo oopsa kwambiri dontho (khambi) lake likhoza kubwelesa zilonda zopweteka kwambiri, kudya chipaso chamuntengowu umafelatu. Utati uyesele kuotcha mtengowu utsi okhawo wa mtengowo umapangisa munthu kusiya kuona. 9. Dziko ndi planet yokhayo imene moto umatha kuyaka. Ma planet enawo nzosatheka chifukwa kulibe oxygen okwanila. 10. Mudzi wina ku Germany, Fuggerei rent sinakwelebe kuchokela 1520. Ndi $1 pachaka (pafupifupi 1800MWK). 11. Mukasecha pa Google kuti "DO A BARELL ROLL" page yonse imazungulira (spinning). 12. China yatulutsa battery ya nuclear imene ukaika mu phone mwanumo, ndiye kuti patha zaka 50 musanatchaje🥱. 13. Nyerere zimagona pafupifupi 9hours patsiku,kuonjezela apo izozi zili ndi mimba ziwiri ina yosungila zakudya zake ina zokudya za amzake. 14. Njoka zazikazi zimatha kusunga ma sperm a amuna kwa zaka 5, amuna ambiri akhoza kugonana ndi njoka zazikazi koma izo zimangolandila ma sperm'wo kumasunga then zimapanga decide kuti nah masperm awa okha agwire ntchito. 15. Malovu athu amakhala ndi ma pathogens amene akhoza kupha mbalame, eya mbalame. Malovu athuwa ndi a toxic kwa zinyama zina monga mbalame. Mbalame itati yachita soka kutela pamlomo kugundana ndi malovu athu, eh! Pamakhala chiopsezo chachikulu kuti ifa chifukwa malovu athu amakhala ndi ma bacteria omwe amapangisa mbalame kumangoyasamula, kukhosomola kwambiri then imafa... Copied from star warelo ```Phosomthumba``` ✍️
Like
3
0 Comments 0 Shares 253 Views 0 Reviews