KODI MUKUDZIWA?
1. Ku Netherlands kuli mlatho wapadera wa agologolo okhaokha womwe unamangidwa kuti aziwoloka msewu kupita tsidya lina la msewu.
2. Ku Netherlands komweko kuli mlatho wina wotchedwa (Moses bridge).
3. Nkhuku ya tambala ili ndi zozitetezera zachilengedwe mmapilikaniro ake zomwe zimamuteteza ku phokoso lake lomwe akhoza kufa nalo. Izi ndizimene zimatchinga mapilikaniro ake akamalira ndipo zili ngati ma (earset).
4. Ubongo wanu ukhoza kugwira ntchito ka 38, 000 trillion pa second imodzi.. Pamene compyuta yapamwamba yamakono ikhoza kugwira ntchito ka 0.002%.
5. Kuti ukhale taxi driver 🚖 ku London, umafunika udziwe njira pafupifupi 320, misewu 25, 000 ndi zizindikiro zokwana 20, 000. Kugwiritsa ntchito GPS ndikoletsedwa.
6. *Expiry date* yomwe imaikidwa pa botolo la pulasiki, limatanthauza za botololo osati madziwo. Madzi paokha samaonongeka koma zinthu zomwe zagwera mmadzimo ndizimene zimaononga madziwo. Choncho zinthu zomwe anapangira botolo la pulasiki zikapanga expiré, zimaononga madzi am'botolomo.
7. Nzere woyera womwe umakhala pakati pa mseu wa phula(white line), unachokera ku design ya mkaka pomwe mkulu wina mu 1911, anaona galimoto lonyamula mkaka ndipo unkadonthera mseu.
8. Mu mphindi 30, thupi lanu limatulutsa nthunzi yoyentha yokwanitsa kuwiritsa 5litres ya madzi.
9. Ku Japan kugona uli pa ntchito nkololeka ndipo zimasonyeza kuti ukugwira ntchito mwakhama osati ulesi monga mmene ena amaganizira.
10. Ukamalankhula ndi munthu nkupezeka munthuyo wayamba kuphethira kwambiri dziwani kuti wasiya kukuonetsani chidwi.
11. Msomba zazikazi zimatha kunamiza zazimuna potulutsa timadzi totchedwa orgasm panthawi ya mating kuti nsomba zazimuna zimve ngati zachitika kenako nsomba yayikazi ija imachokapo kukapeza bwezi lina labwino loti ikhoza kusangalataidwa naye.
12. Mu chilengedwe chonse mitengo ndi yofunika kuposa miyala ya mtengo wa patali ya diamond.
13. Zikhadabo ndi tsitsi la mayi oyembekezera zimakula msanga mosiyana ndimmene zimakhalira akakhala bwinobwino.
14. Udzudzu umakhala ndi moyo kwa ma sabata awiri okha.
15. Udzudzu umakonda munthu yemwe wangodya kumene nthochi kapena amene wamwa mowa. Munthu ameneso magazi ake ali mu group (ô) udzudzu umamuthamangira ameneyo.
16. Udzudzu umakula kuchoka kudzira kufika pa waukulu mu masiku anayi okha.
17. Lilime la nsomba ya blue whale litha kulemera mofanana ndi njovu yaing’ono.
18. Amphaka amakhulupirira ndi kukonda munthu podzigundanitsa ku munthuyo ndi mutu wake komanso thupi lake lonse.
19. A bulu( horses), amatha kuona bwino kufika pa 360 degree akaphethira nkuona paulendo umodzi.
20. Agalu amatha kuzindikira matenda a khansa pa thupi lambuyawo kapena pa munthu wina.
21. Nkhuku ndi imene imadyedwa ndi munthu isanabadwe komanso isanafe.( osasokonezeka ganizani mozama kenako mubwereso).
22. Mtchetche zimalawa chakudya ndi mapazi awo.
23. Nyama za Kamelo zikhoza kufika miyezi 6 osadya kapena kumwa madzi.