Making people understand the society they live in and also the society of other people without being eurocentric and understand things in a relativism way
Недавние обновления
-
KODI MUKUDZIWA?
1. Ku Netherlands kuli mlatho wapadera wa agologolo okhaokha womwe unamangidwa kuti aziwoloka msewu kupita tsidya lina la msewu.
2. Ku Netherlands komweko kuli mlatho wina wotchedwa (Moses bridge).
3. Nkhuku ya tambala ili ndi zozitetezera zachilengedwe mmapilikaniro ake zomwe zimamuteteza ku phokoso lake lomwe akhoza kufa nalo. Izi ndizimene zimatchinga mapilikaniro ake akamalira ndipo zili ngati ma (earset).
4. Ubongo wanu ukhoza kugwira ntchito ka 38, 000 trillion pa second imodzi.. Pamene compyuta yapamwamba yamakono ikhoza kugwira ntchito ka 0.002%.
5. Kuti ukhale taxi driver 🚖 ku London, umafunika udziwe njira pafupifupi 320, misewu 25, 000 ndi zizindikiro zokwana 20, 000. Kugwiritsa ntchito GPS ndikoletsedwa.
6. *Expiry date* yomwe imaikidwa pa botolo la pulasiki, limatanthauza za botololo osati madziwo. Madzi paokha samaonongeka koma zinthu zomwe zagwera mmadzimo ndizimene zimaononga madziwo. Choncho zinthu zomwe anapangira botolo la pulasiki zikapanga expiré, zimaononga madzi am'botolomo.
7. Nzere woyera womwe umakhala pakati pa mseu wa phula(white line), unachokera ku design ya mkaka pomwe mkulu wina mu 1911, anaona galimoto lonyamula mkaka ndipo unkadonthera mseu.
8. Mu mphindi 30, thupi lanu limatulutsa nthunzi yoyentha yokwanitsa kuwiritsa 5litres ya madzi.
9. Ku Japan kugona uli pa ntchito nkololeka ndipo zimasonyeza kuti ukugwira ntchito mwakhama osati ulesi monga mmene ena amaganizira.
10. Ukamalankhula ndi munthu nkupezeka munthuyo wayamba kuphethira kwambiri dziwani kuti wasiya kukuonetsani chidwi.
11. Msomba zazikazi zimatha kunamiza zazimuna potulutsa timadzi totchedwa orgasm panthawi ya mating kuti nsomba zazimuna zimve ngati zachitika kenako nsomba yayikazi ija imachokapo kukapeza bwezi lina labwino loti ikhoza kusangalataidwa naye.
12. Mu chilengedwe chonse mitengo ndi yofunika kuposa miyala ya mtengo wa patali ya diamond.
13. Zikhadabo ndi tsitsi la mayi oyembekezera zimakula msanga mosiyana ndimmene zimakhalira akakhala bwinobwino.
14. Udzudzu umakhala ndi moyo kwa ma sabata awiri okha.
15. Udzudzu umakonda munthu yemwe wangodya kumene nthochi kapena amene wamwa mowa. Munthu ameneso magazi ake ali mu group (ô) udzudzu umamuthamangira ameneyo.
16. Udzudzu umakula kuchoka kudzira kufika pa waukulu mu masiku anayi okha.
17. Lilime la nsomba ya blue whale litha kulemera mofanana ndi njovu yaing’ono.
18. Amphaka amakhulupirira ndi kukonda munthu podzigundanitsa ku munthuyo ndi mutu wake komanso thupi lake lonse.
19. A bulu( horses), amatha kuona bwino kufika pa 360 degree akaphethira nkuona paulendo umodzi.
20. Agalu amatha kuzindikira matenda a khansa pa thupi lambuyawo kapena pa munthu wina.
21. Nkhuku ndi imene imadyedwa ndi munthu isanabadwe komanso isanafe.( osasokonezeka ganizani mozama kenako mubwereso).
22. Mtchetche zimalawa chakudya ndi mapazi awo.
23. Nyama za Kamelo zikhoza kufika miyezi 6 osadya kapena kumwa madzi.
KODI MUKUDZIWA? 1. Ku Netherlands kuli mlatho wapadera wa agologolo okhaokha womwe unamangidwa kuti aziwoloka msewu kupita tsidya lina la msewu. 2. Ku Netherlands komweko kuli mlatho wina wotchedwa (Moses bridge). 3. Nkhuku ya tambala ili ndi zozitetezera zachilengedwe mmapilikaniro ake zomwe zimamuteteza ku phokoso lake lomwe akhoza kufa nalo. Izi ndizimene zimatchinga mapilikaniro ake akamalira ndipo zili ngati ma (earset). 4. Ubongo wanu ukhoza kugwira ntchito ka 38, 000 trillion pa second imodzi.. Pamene compyuta yapamwamba yamakono ikhoza kugwira ntchito ka 0.002%. 5. Kuti ukhale taxi driver 🚖 ku London, umafunika udziwe njira pafupifupi 320, misewu 25, 000 ndi zizindikiro zokwana 20, 000. Kugwiritsa ntchito GPS ndikoletsedwa. 6. *Expiry date* yomwe imaikidwa pa botolo la pulasiki, limatanthauza za botololo osati madziwo. Madzi paokha samaonongeka koma zinthu zomwe zagwera mmadzimo ndizimene zimaononga madziwo. Choncho zinthu zomwe anapangira botolo la pulasiki zikapanga expiré, zimaononga madzi am'botolomo. 7. Nzere woyera womwe umakhala pakati pa mseu wa phula(white line), unachokera ku design ya mkaka pomwe mkulu wina mu 1911, anaona galimoto lonyamula mkaka ndipo unkadonthera mseu. 8. Mu mphindi 30, thupi lanu limatulutsa nthunzi yoyentha yokwanitsa kuwiritsa 5litres ya madzi. 9. Ku Japan kugona uli pa ntchito nkololeka ndipo zimasonyeza kuti ukugwira ntchito mwakhama osati ulesi monga mmene ena amaganizira. 10. Ukamalankhula ndi munthu nkupezeka munthuyo wayamba kuphethira kwambiri dziwani kuti wasiya kukuonetsani chidwi. 11. Msomba zazikazi zimatha kunamiza zazimuna potulutsa timadzi totchedwa orgasm panthawi ya mating kuti nsomba zazimuna zimve ngati zachitika kenako nsomba yayikazi ija imachokapo kukapeza bwezi lina labwino loti ikhoza kusangalataidwa naye. 12. Mu chilengedwe chonse mitengo ndi yofunika kuposa miyala ya mtengo wa patali ya diamond. 13. Zikhadabo ndi tsitsi la mayi oyembekezera zimakula msanga mosiyana ndimmene zimakhalira akakhala bwinobwino. 14. Udzudzu umakhala ndi moyo kwa ma sabata awiri okha. 15. Udzudzu umakonda munthu yemwe wangodya kumene nthochi kapena amene wamwa mowa. Munthu ameneso magazi ake ali mu group (ô) udzudzu umamuthamangira ameneyo. 16. Udzudzu umakula kuchoka kudzira kufika pa waukulu mu masiku anayi okha. 17. Lilime la nsomba ya blue whale litha kulemera mofanana ndi njovu yaing’ono. 18. Amphaka amakhulupirira ndi kukonda munthu podzigundanitsa ku munthuyo ndi mutu wake komanso thupi lake lonse. 19. A bulu( horses), amatha kuona bwino kufika pa 360 degree akaphethira nkuona paulendo umodzi. 20. Agalu amatha kuzindikira matenda a khansa pa thupi lambuyawo kapena pa munthu wina. 21. Nkhuku ndi imene imadyedwa ndi munthu isanabadwe komanso isanafe.( osasokonezeka ganizani mozama kenako mubwereso). 22. Mtchetche zimalawa chakudya ndi mapazi awo. 23. Nyama za Kamelo zikhoza kufika miyezi 6 osadya kapena kumwa madzi.Войдите, чтобы отмечать, делиться и комментировать! -
KODI MUKUDZIWA??
```Phosomthumba``` ✍️
1. Pali kampani ina ku USA imene ikuti ipeleka $10, 000 (16,825,598.91 MWK) kwa munthu amene atakhale mwezi osasewelesa foni yake.
2. Ubongo wathu umayamba kukhwinyika (shrink) tikamafika zaka za m'mma 30s/40s.
3. Anonychia ndi medical condition imene munthu amabadwa, kukula opanda zikhadabo.
4. Chocolate, cheese komanso red wine ati zimathandiza kuti munthu akhale ndi moyo wautali. A science amatelo.
5. Ku India kuli temple inayake imene galu amapeleka madalitso anthu akamutuluka mu temple'mu.
6. Munthu olemera kwambiri padziko lonse lapansi anali Mansa Musa ndipo chuma chake kufikila lero palibe amayandikilako $400, 000, 000, 000.
7. Acid amene amapezeka m'mimba mwathu ali ndi kuthekela kosungunla lezala.
8. Mtengo wa machineel ndi mtengo oopsa kwambiri dontho (khambi) lake likhoza kubwelesa zilonda zopweteka kwambiri, kudya chipaso chamuntengowu umafelatu. Utati uyesele kuotcha mtengowu utsi okhawo wa mtengowo umapangisa munthu kusiya kuona.
9. Dziko ndi planet yokhayo imene moto umatha kuyaka. Ma planet enawo nzosatheka chifukwa kulibe oxygen okwanila.
10. Mudzi wina ku Germany, Fuggerei rent sinakwelebe kuchokela 1520. Ndi $1 pachaka (pafupifupi 1800MWK).
11. Mukasecha pa Google kuti "DO A BARELL ROLL" page yonse imazungulira (spinning).
12. China yatulutsa battery ya nuclear imene ukaika mu phone mwanumo, ndiye kuti patha zaka 50 musanatchaje🥱.
13. Nyerere zimagona pafupifupi 9hours patsiku,kuonjezela apo izozi zili ndi mimba ziwiri ina yosungila zakudya zake ina zokudya za amzake.
14. Njoka zazikazi zimatha kusunga ma sperm a amuna kwa zaka 5, amuna ambiri akhoza kugonana ndi njoka zazikazi koma izo zimangolandila ma sperm'wo kumasunga then zimapanga decide kuti nah masperm awa okha agwire ntchito.
15. Malovu athu amakhala ndi ma pathogens amene akhoza kupha mbalame, eya mbalame. Malovu athuwa ndi a toxic kwa zinyama zina monga mbalame. Mbalame itati yachita soka kutela pamlomo kugundana ndi malovu athu, eh! Pamakhala chiopsezo chachikulu kuti ifa chifukwa malovu athu amakhala ndi ma bacteria omwe amapangisa mbalame kumangoyasamula, kukhosomola kwambiri then imafa...
Copied from star warelo ```Phosomthumba``` ✍️KODI MUKUDZIWA?? ```Phosomthumba``` ✍️ 1. Pali kampani ina ku USA imene ikuti ipeleka $10, 000 (16,825,598.91 MWK) kwa munthu amene atakhale mwezi osasewelesa foni yake. 2. Ubongo wathu umayamba kukhwinyika (shrink) tikamafika zaka za m'mma 30s/40s. 3. Anonychia ndi medical condition imene munthu amabadwa, kukula opanda zikhadabo. 4. Chocolate, cheese komanso red wine ati zimathandiza kuti munthu akhale ndi moyo wautali. A science amatelo. 5. Ku India kuli temple inayake imene galu amapeleka madalitso anthu akamutuluka mu temple'mu. 6. Munthu olemera kwambiri padziko lonse lapansi anali Mansa Musa ndipo chuma chake kufikila lero palibe amayandikilako $400, 000, 000, 000. 7. Acid amene amapezeka m'mimba mwathu ali ndi kuthekela kosungunla lezala. 8. Mtengo wa machineel ndi mtengo oopsa kwambiri dontho (khambi) lake likhoza kubwelesa zilonda zopweteka kwambiri, kudya chipaso chamuntengowu umafelatu. Utati uyesele kuotcha mtengowu utsi okhawo wa mtengowo umapangisa munthu kusiya kuona. 9. Dziko ndi planet yokhayo imene moto umatha kuyaka. Ma planet enawo nzosatheka chifukwa kulibe oxygen okwanila. 10. Mudzi wina ku Germany, Fuggerei rent sinakwelebe kuchokela 1520. Ndi $1 pachaka (pafupifupi 1800MWK). 11. Mukasecha pa Google kuti "DO A BARELL ROLL" page yonse imazungulira (spinning). 12. China yatulutsa battery ya nuclear imene ukaika mu phone mwanumo, ndiye kuti patha zaka 50 musanatchaje🥱. 13. Nyerere zimagona pafupifupi 9hours patsiku,kuonjezela apo izozi zili ndi mimba ziwiri ina yosungila zakudya zake ina zokudya za amzake. 14. Njoka zazikazi zimatha kusunga ma sperm a amuna kwa zaka 5, amuna ambiri akhoza kugonana ndi njoka zazikazi koma izo zimangolandila ma sperm'wo kumasunga then zimapanga decide kuti nah masperm awa okha agwire ntchito. 15. Malovu athu amakhala ndi ma pathogens amene akhoza kupha mbalame, eya mbalame. Malovu athuwa ndi a toxic kwa zinyama zina monga mbalame. Mbalame itati yachita soka kutela pamlomo kugundana ndi malovu athu, eh! Pamakhala chiopsezo chachikulu kuti ifa chifukwa malovu athu amakhala ndi ma bacteria omwe amapangisa mbalame kumangoyasamula, kukhosomola kwambiri then imafa... Copied from star warelo ```Phosomthumba``` ✍️ -
A former enslaved person who became the most prominent leader of the Haitian Revolution, Toussaint Louverture helped establish the world’s first independent Black republic in 1804. He is now known as “The Father of Haiti.”
A former enslaved person who became the most prominent leader of the Haitian Revolution, Toussaint Louverture helped establish the world’s first independent Black republic in 1804. He is now known as “The Father of Haiti.” -
Dr. Joseph Murphy was a prominent New Thought minister and author who is best known for his work in the field of self-help and spiritual growth. He was born in Ireland in 1898 and later moved to the United States, where he became a minister in the Divine Science Church.
Dr. Murphy's teachings were heavily influenced by the concept of the subconscious mind and its power to shape our lives. He believed that by changing our thoughts and beliefs, we could transform our circumstances and achieve success, happiness, and prosperity.
One of Dr. Murphy's most famous works is the book "The Power of Your Subconscious Mind," which was first published in 1963. In this book, he explores how the subconscious mind works, and offers practical techniques for harnessing its power to overcome challenges and manifest our desires.
Dr. Murphy's teachings emphasize the importance of positive thinking, affirmations, visualization, and the power of faith in creating the life we want. He believed that by aligning our conscious and subconscious minds, we could tap into our inner potential and achieve our goals.
Throughout his career, Dr. Joseph Murphy wrote numerous books, delivered lectures, and conducted workshops on topics related to personal development, spiritual growth, and the power of the mind. His work continues to inspire and influence people seeking to improve their lives and unlock their full potential.Dr. Joseph Murphy was a prominent New Thought minister and author who is best known for his work in the field of self-help and spiritual growth. He was born in Ireland in 1898 and later moved to the United States, where he became a minister in the Divine Science Church. Dr. Murphy's teachings were heavily influenced by the concept of the subconscious mind and its power to shape our lives. He believed that by changing our thoughts and beliefs, we could transform our circumstances and achieve success, happiness, and prosperity. One of Dr. Murphy's most famous works is the book "The Power of Your Subconscious Mind," which was first published in 1963. In this book, he explores how the subconscious mind works, and offers practical techniques for harnessing its power to overcome challenges and manifest our desires. Dr. Murphy's teachings emphasize the importance of positive thinking, affirmations, visualization, and the power of faith in creating the life we want. He believed that by aligning our conscious and subconscious minds, we could tap into our inner potential and achieve our goals. Throughout his career, Dr. Joseph Murphy wrote numerous books, delivered lectures, and conducted workshops on topics related to personal development, spiritual growth, and the power of the mind. His work continues to inspire and influence people seeking to improve their lives and unlock their full potential. -
Gotham 05 added 3 фото & является Чтение Thaipusam is a Hindu festival celebrated by the Tamil community, particularly in countries like India, Malaysia, Singapore, Sri Lanka, and Mauritius. The festival is dedicated to Lord Murugan, also known as Kartikeya or Skanda, who is the Hindu god of war
-
Больше